Home Politics Phungu wa dera la kum’mwera cha ku m’mawa kwa mzinda wa Blantyre Sameer Suleiman apambana pachisankho chachipulula atogonjeza a Wild Ndipo yemwe ndi mfumu yakale ya mzinda wa Blantyre

Phungu wa dera la kum’mwera cha ku m’mawa kwa mzinda wa Blantyre Sameer Suleiman apambana pachisankho chachipulula atogonjeza a Wild Ndipo yemwe ndi mfumu yakale ya mzinda wa Blantyre

by Kingsley Sowa
0 comments

Phungu wanyumba yamalamulo kudera la Kum’mwera- chakum’mawa Kwa mzinda wa Blantyre a Sameer Suleiman apambana pachisankho chachipululala chomwe chachitika kuderali lachiwiri.

A Suleiman apambana pachisankhochi ndi mavoti 458 pamene yemwe amapikisana nawo a Wild Ndipo apeza mavoti 17.

Izi zikutanthauza kuti a Suleiman ndi omwe adzaimire pampando waphungu wanyumba yamalamulo pachipani Cha DPP kudera la Chigumula-BCA -Club Banana pachisankhochi chapa 16 September Chaka chino.

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00