Mtsogoleri wachipani cha Malawi congress Dr. Lazarus Mccarthy Chakwera avomereza kugonja pachisankho chomwe chinachitika pa 16 September chaka chino. Dr. Chakwera avomereza …
Politics
-
-
Malawi Congress party aspiring Member of Parliament for Blantyre-Chichiri-Misesa Enala Shaba has pledged to continue renovating bridges in the area in order …
-
Yemwe akuima payekha pampando wa phungu kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa a Paul Kachitsa adzudzula mchitidwe wa andale ena opereka katundu kwa anthu ovota …
-
Politics
Opposition Democratic progressive party again promise to bail out Malawians from challenges rocking the country.
The opposition Democratic progressive party-DPP has again promised to bail out Malawians from challenges rocking the country. DPP Vice President for the …
-
Politics
Atsogoleri omwe akuimira kudera Blantyre-Chichiri -Misesa agwirizana zochita misonkhano yamtendere.
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana mdziko muno la NICE-TRUST lalangiza mzika zadziko lino kuvotera atsogoleri okhawo omwe ali ndi masomphenya otukula madera …
-
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana la NICE Trust lakumbutsa anthu omwe aonetsa chidwi choimila pachisankho chapa 16 September kulimbiikitsa mtendere pamene nyengo …
-
Khansala wadera la Chigumula a Wild Ndipo omwe anagonja pachisankho chachipulula kwa a Sameer Suleiman pachipani cha Democratic progressive-DPP ati ayimila derali …
-
Politics
A Enala Yesaya achipani cha MCP apambana pazisankho zachipulula za aphungu kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa.
Yemwe akuimila paudindo waphungu kudera Blantyre-Chichiri-Misesa muchipani cha Malawi congress-MCP Enala Yesaya wapambana pachisankho chachipulula chomwe chachitika lachitatu pasukulu ya pulaimale ya …
-
Politics
Phungu yemwe akuyimira kudela la Blantyre-Chichiri-Misesa walonjeza zitukuko kudelali akazapambana chisankho mwezi wa September
Yemwe akuimira pampando wa phungu wanyumba yamalamulo kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa Themba Mkandawire wayamba ntchito yokambirana ndi mafumu pazina mwa zitukuko zomwe akufuna …
-
Politics
Mtsogoleri wachipani chomwe changoyamba kumene cha Peoples Voice -PVP a Laurence Nkuzi Banda adzudzula utsogoleri wadziko lino polephera kugwiritsa ntchito zipangizo zomwe dziko lino lili nazo potukula chuma cha dziko lino.
Malinga ndi a Nkuzi Banda a Malawi akupitilira kukumana ndi mavuto osiyanasiyana monga vuto la njala, kusowa kwa mafuta agalimoto komanso kukwera …