A Total of 354 recruited immigration officers who have passed out on Friday 30th May 2025 in Blantyre have been challenged to …
May 2025
-
-
Politics
A Enala Yesaya achipani cha MCP apambana pazisankho zachipulula za aphungu kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa.
Yemwe akuimila paudindo waphungu kudera Blantyre-Chichiri-Misesa muchipani cha Malawi congress-MCP Enala Yesaya wapambana pachisankho chachipulula chomwe chachitika lachitatu pasukulu ya pulaimale ya …
-
Health
Tikufuna kukhazikitsa gulu lina lothanzira anthu odwala nthenda ya khansa ku Blantyre-Cancer Survivors Quest
Bungwe loyang’anira anthu omwe anapulumuka kunthenda ya khansa la Cancer survivors Quest lati likukonza zogwira ntchito yozindikilitsa anthu komanso kukhazikitsa gulu la …
-
A snap survey by eagle online has revealed that this year’s primary school leaving certificate of educations have started well. Students with …
-
Politics
Phungu yemwe akuyimira kudela la Blantyre-Chichiri-Misesa walonjeza zitukuko kudelali akazapambana chisankho mwezi wa September
Yemwe akuimira pampando wa phungu wanyumba yamalamulo kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa Themba Mkandawire wayamba ntchito yokambirana ndi mafumu pazina mwa zitukuko zomwe akufuna …
-
Apolisi ku Limbe akusunga mchitolokosi cha apolisi bambo wazaka 24 Emmanuel Davie pomuganizira kuti amanamiza anthu kuti ndi msilikali wa Malawi Defense …
-
The Malawi confederation of Chambers of commerce and industry-MCCCI says more than 200 companies have shown interest to participate in this year’s …
-
Kalinda life care foundation has expressed the need for young people to take a leading role in creating a conducive environment for …
-
Sports
Bungwe loyang’anira masewero achisodzera mdziko muno lati likukonza ndondomeko yotsikimiza zaka za osewera league yachaka chino isanayambe
Bungwe loyang’anira masewero achisodzera mdziko muno lati likukonza zochititsa ntchito yotsikimiza zaka za osewera league yachaka chino isanayambe. Mlembi wamkulu wabungweli Rabson …
-
Education
Malawi University of Business and Applied Sciences(MUBAS) partners with university of strathclyde Glasgow of Scotland
Building strong partnerships with other International higher learning institutions has been singled out as one of the contributing factor to promote education …