Home Featured Police ya Limbe yapempha anthu okhala kumadera omwe alipansi pa polisiyi kukhala atcheru pamene akhristu akukonzekera nyengo ya Pasaka yomwe ndi nthawi yokumbukira mazunzo, imfa komanso kuuka kwa Yesu khristu.

Police ya Limbe yapempha anthu okhala kumadera omwe alipansi pa polisiyi kukhala atcheru pamene akhristu akukonzekera nyengo ya Pasaka yomwe ndi nthawi yokumbukira mazunzo, imfa komanso kuuka kwa Yesu khristu.

by Kingsley Sowa
0 comments

Mu nyengoyi akhristu amipingo yosiyanasiyana amakonza zochitika monga njira ya mtanda, ulendo wa ndawala, Tsiku la Kanjedza komanso misonkhano yolamilikira kumadera osiyanasiyana. 

M’neneri wa polisi ya Limbe Sergeant Aubrey Singanyama wati pamene akhristu akukumbukira nyengoyi akubanso nawo amapezelapo mwayi ochita zaupandu.

Sergeant Singanyama wati monga mwa udindo wawo oteteza miyoyo ndi katundu wa anthu, apolisi alimbikitsa njira zingapo monga kukhazikitsa zipata zapamsewu komanso ntchito yoyendera madera osiyanasiyana omwe ali pansi pa polisiyi.

Iwo apitiriza kukumbutsa anthuwa za udindo waukulu omwe ali nawo pawokha posamalira ndi kuteteza katundu wawo ndi kupewa kuyenda nthawi yolakwika mwa zina.

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00

Connection Information

To perform the requested action, WordPress needs to access your web server. Please enter your FTP credentials to proceed. If you do not remember your credentials, you should contact your web host.

Connection Type