Mtsogoleri wachipani cha Malawi congress Dr. Lazarus Mccarthy Chakwera avomereza kugonja pachisankho chomwe chinachitika pa 16 September chaka chino. Dr. Chakwera avomereza…
Mtsogoleri wachipani cha Malawi congress Dr. Lazarus Mccarthy Chakwera avomereza kugonja pachisankho chomwe chinachitika pa 16 September chaka chino. Dr. Chakwera avomereza…
Malawi Congress party aspiring Member of Parliament for Blantyre-Chichiri-Misesa Enala Shaba has pledged to continue renovating bridges in the area in order…
Yemwe akuima payekha pampando wa phungu kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa a Paul Kachitsa adzudzula mchitidwe wa andale ena opereka katundu kwa anthu ovota…
The opposition Democratic progressive party-DPP has again promised to bail out Malawians from challenges rocking the country. DPP Vice President for the…
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana mdziko muno la NICE-TRUST lalangiza mzika zadziko lino kuvotera atsogoleri okhawo omwe ali ndi masomphenya otukula madera…
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana la NICE Trust lakumbutsa anthu omwe aonetsa chidwi choimila pachisankho chapa 16 September kulimbiikitsa mtendere pamene nyengo…
Khansala wadera la Chigumula a Wild Ndipo omwe anagonja pachisankho chachipulula kwa a Sameer Suleiman pachipani cha Democratic progressive-DPP ati ayimila derali…
Yemwe akuimila paudindo waphungu kudera Blantyre-Chichiri-Misesa muchipani cha Malawi congress-MCP Enala Yesaya wapambana pachisankho chachipulula chomwe chachitika lachitatu pasukulu ya pulaimale ya…
Yemwe akuimira pampando wa phungu wanyumba yamalamulo kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa Themba Mkandawire wayamba ntchito yokambirana ndi mafumu pazina mwa zitukuko zomwe akufuna…
Malinga ndi a Nkuzi Banda a Malawi akupitilira kukumana ndi mavuto osiyanasiyana monga vuto la njala, kusowa kwa mafuta agalimoto komanso kukwera…