Mtsogoleri wachipani cha Malawi congress Dr. Lazarus Mccarthy Chakwera avomereza kugonja pachisankho chomwe chinachitika pa 16 September chaka chino. Dr. Chakwera avomereza …
National
-
-
Motorcycle operators have been reminded to register their bikes and obtain licenses before the end of the last phase of registration window …
-
Gulu la mzika zokhudzidwa la union of concerned citizens’ lalimbikitsa a Malawi kukhala a mtendere pamene tsiku loponya voti likuwandikila. Izi zayankhulidwa …
-
Government through the ministry of Homeland security has assured Malawians of smooth issuing and printing of passport services as the department of …
-
National
Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti atsogoleri amipingo maka akumadera akumidzi ali ndi chokudya chokwanira, bungwe la Chiyembekezo center for transformation lalimbikitsa ntchito yophunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo zamomwe angapangile feteleza pogwiritsa ntchito zipangizo zopezeka m’madera mwawo m’boma la Phalombe.
Lachiwiri pa 17 June, Bungweli laphunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo makumi awiri ochokera mipingo yosiyanasiyana omwe ali pansi pagulu la Leyman Pastors …
-
National
Newly recruited immigration officers urged to serve the citizenry with integrity – Minister Ezekiel Ching’oma
A Total of 354 recruited immigration officers who have passed out on Friday 30th May 2025 in Blantyre have been challenged to …
-
National
Mfumu Kapeni yalimbikitsa chitukuko mu mzinda wa Blantyre pofuna kufikira maloto a chaka cha 2063
Mfumu yaikulu Kapeni ya mumzinda wa Blantyre yati ntchito yozindikiritsa anthu za nkhani ya chitukuko ndi yofunika kwambiri polimbikitsa a Malawi kutenga …
-
National
NICE Trust yalimbikitsa onse oyenera kuvota pachisankho kutenga gawo pakampeni yotsikimizira maina mukaundula wachisankho.
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana mdziko muno la NICE Trust lalimbikitsa anthu omwe ali oyenera kuponya voti pachisankho chachaka chino kuti atenge …
-
National
DoDMA Challenges the citizenry to asses personal budgeting to avoid rooming hunger in the year 2025-2026.
Director of Disaster Preparedness and Response for DODMA Moses Chimphepo has said this in Nchinji district during the distribution of maize to …