Tikufuna kukhazikitsa gulu lina lothanzira anthu odwala nthenda ya khansa ku Blantyre-Cancer Survivors Quest
Bungwe loyang’anira anthu omwe anapulumuka kunthenda ya khansa la Cancer survivors Quest lati likukonza zogwira ntchito yozindikilitsa anthu komanso kukhazikitsa gulu la…