Polisi ya Limbe yati chiwelengero cha ngozi zapamsewu chatsika ndi 22 pelesenti m’miyezi isanu ndi umodzi ya chaka chino kuyerekeza ndi nyengo …
Category:
Crime
-
-
Bambo wa zaka 62, Frank Kayuni wafa ataziombela ndi mfuti m’mawa wa lachiwiri pa 15 July pachipatala cha Mwaiwathu mumzinda wa Blantyre …
-
Crime
Polisi ya Limbe yatsimikiza za imfa ya bamboo wa zaka 66 Davison Tambala yemwe wazipha yekha kudera la mfumu Chipagala ku BCA mu mzinda wa Blantyre.
Malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Limbe Sub Inspector Sam Kadyole, thupi la bambo Tambala linapezedwa likulendewera kudenga la nyumba …
-
Apolisi ku Limbe akusunga mchitolokosi cha apolisi bambo wazaka 24 Emmanuel Davie pomuganizira kuti amanamiza anthu kuti ndi msilikali wa Malawi Defense …