Phungu wa dera la kum’mwera cha ku m’mawa kwa mzinda wa Blantyre Sameer Suleiman apambana pachisankho chachipulula atogonjeza a Wild Ndipo yemwe ndi mfumu yakale ya mzinda wa Blantyre
Phungu wanyumba yamalamulo kudera la Kum’mwera- chakum’mawa Kwa mzinda wa Blantyre a Sameer Suleiman apambana pachisankho chachipululala chomwe chachitika kuderali lachiwiri. A…