Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti chitetezo ndi chokhwima kudera la Limbe, kampani ya Premier Bet lachisanu yapereka thandizo la ndalama zokwana 1…
Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti chitetezo ndi chokhwima kudera la Limbe, kampani ya Premier Bet lachisanu yapereka thandizo la ndalama zokwana 1…
Malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Limbe Sub Inspector Sam Kadyole, thupi la bambo Tambala linapezedwa likulendewera kudenga la nyumba…
Lachiwiri pa 17 June, Bungweli laphunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo makumi awiri ochokera mipingo yosiyanasiyana omwe ali pansi pagulu la Leyman Pastors…
Gulu la ophunzira omwe anaphunzira pasukulu ya sekondale ya Mulanje muzaka zapakati pa 2008 ndi 2011 lati likukonza zopeza njira zosiyanasiyana zopezera…
Yemwe akuimira pa mpando wa khansala woima payekha kudera la BCA-Chigumula mumzinda wa Blantyre a Sadana Bakili atsindika kufunika koti atsogoleri azitengapo…
A Total of 354 recruited immigration officers who have passed out on Friday 30th May 2025 in Blantyre have been challenged to…
Yemwe akuimila paudindo waphungu kudera Blantyre-Chichiri-Misesa muchipani cha Malawi congress-MCP Enala Yesaya wapambana pachisankho chachipulula chomwe chachitika lachitatu pasukulu ya pulaimale ya…
Bungwe loyang’anira anthu omwe anapulumuka kunthenda ya khansa la Cancer survivors Quest lati likukonza zogwira ntchito yozindikilitsa anthu komanso kukhazikitsa gulu la…
A snap survey by eagle online has revealed that this year’s primary school leaving certificate of educations have started well. Students with…
Yemwe akuimira pampando wa phungu wanyumba yamalamulo kudera la Blantyre-Chichiri-Misesa Themba Mkandawire wayamba ntchito yokambirana ndi mafumu pazina mwa zitukuko zomwe akufuna…