June 2025

Khansala wadera la Chigumula a Wild Ndipo omwe anagonja pachisankho chachipulula kwa a Sameer Suleiman pachipani cha Democratic progressive-DPP ati ayimila derali…

Read more

Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti chitetezo ndi chokhwima kudera la Limbe, kampani ya Premier Bet lachisanu yapereka thandizo la ndalama zokwana 1…

Read more

Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti atsogoleri amipingo maka akumadera akumidzi ali ndi chokudya chokwanira, bungwe la Chiyembekezo center for transformation lalimbikitsa ntchito yophunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo zamomwe angapangile feteleza pogwiritsa ntchito zipangizo zopezeka m’madera mwawo m’boma la Phalombe.

Lachiwiri pa 17 June, Bungweli laphunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo makumi awiri ochokera mipingo yosiyanasiyana omwe ali pansi pagulu la Leyman Pastors…

Read more