Khansala wadera la Chigumula a Wild Ndipo omwe anagonja pachisankho chachipulula kwa a Sameer Suleiman pachipani cha Democratic progressive-DPP ati ayimila derali …
June 2025
-
-
Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti chitetezo ndi chokhwima kudera la Limbe, kampani ya Premier Bet lachisanu yapereka thandizo la ndalama zokwana 1 …
-
Crime
Polisi ya Limbe yatsimikiza za imfa ya bamboo wa zaka 66 Davison Tambala yemwe wazipha yekha kudera la mfumu Chipagala ku BCA mu mzinda wa Blantyre.
Malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Limbe Sub Inspector Sam Kadyole, thupi la bambo Tambala linapezedwa likulendewera kudenga la nyumba …
-
National
Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti atsogoleri amipingo maka akumadera akumidzi ali ndi chokudya chokwanira, bungwe la Chiyembekezo center for transformation lalimbikitsa ntchito yophunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo zamomwe angapangile feteleza pogwiritsa ntchito zipangizo zopezeka m’madera mwawo m’boma la Phalombe.
Lachiwiri pa 17 June, Bungweli laphunzitsa abusa komanso atsogoleri amipingo makumi awiri ochokera mipingo yosiyanasiyana omwe ali pansi pagulu la Leyman Pastors …
-
Education
Gulu la ophunzira akale pasukulu ya Mulanje Secondary agwirana manja pothandizira ana osowa apa sukuluyi
Gulu la ophunzira omwe anaphunzira pasukulu ya sekondale ya Mulanje muzaka zapakati pa 2008 ndi 2011 lati likukonza zopeza njira zosiyanasiyana zopezera …
-
Yemwe akuimira pa mpando wa khansala woima payekha kudera la BCA-Chigumula mumzinda wa Blantyre a Sadana Bakili atsindika kufunika koti atsogoleri azitengapo …